Salimo 59:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, Mulungu wa makamu, ndinu Mulungu wa Isiraeli.+Nyamukani ndi kuweruza mitundu yonse ya anthu.+Musakomere mtima aliyense woipa ndi wachiwembu.+ [Seʹlah.] Salimo 69:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Wonjezerani zolakwa pa zolakwa zawo,+Ndipo inu musawaone monga olungama.+ Yeremiya 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Yehova mukudziwa bwino chiwembu chimene andikonzera kuti andiphe.+ Musakhululukire* cholakwa chawo, ndipo musafafanize tchimo lawolo pamaso panu. Koma iwo apunthwe pamaso panu.+ Muwachitire zimenezi pa nthawi ya mkwiyo wanu.+ 2 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+
5 Inu Yehova, Mulungu wa makamu, ndinu Mulungu wa Isiraeli.+Nyamukani ndi kuweruza mitundu yonse ya anthu.+Musakomere mtima aliyense woipa ndi wachiwembu.+ [Seʹlah.]
23 Koma inu Yehova mukudziwa bwino chiwembu chimene andikonzera kuti andiphe.+ Musakhululukire* cholakwa chawo, ndipo musafafanize tchimo lawolo pamaso panu. Koma iwo apunthwe pamaso panu.+ Muwachitire zimenezi pa nthawi ya mkwiyo wanu.+
14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+