Nehemiya 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo ena anali kunena kuti: “Nthawi ya njala, tikumapereka minda yathu ya tirigu, minda yathu ya mpesa ndi nyumba zathu monga chikole+ kuti tipeze chakudya.”
3 Ndipo ena anali kunena kuti: “Nthawi ya njala, tikumapereka minda yathu ya tirigu, minda yathu ya mpesa ndi nyumba zathu monga chikole+ kuti tipeze chakudya.”