2 Samueli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+ Salimo 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+ Yesaya 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma munthu wopatsa amapereka malangizo okhudza kupatsa, ndipo iyeyo amapitiriza kukhala wopatsa.+ Afilipi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamaganizire zofuna zanu zokha,+ koma muziganiziranso zofuna za ena.+ 1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+
7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndithu, ndikusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani bambo ako.+ Ndikubwezera munda wonse+ wa Sauli agogo ako ndipo iweyo uzidya mkate patebulo langa nthawi zonse.”+
21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+