Miyambo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu osiya chilamulo akamatamanda munthu woipa,+ anthu amene amasunga chilamulo amawaukira.+ Yohane 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+ 1 Yohane 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ndi ochokera m’dziko,+ n’chifukwa chake amalankhula zochokera m’dziko ndipo dziko limawamvera.+
19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+
5 Iwo ndi ochokera m’dziko,+ n’chifukwa chake amalankhula zochokera m’dziko ndipo dziko limawamvera.+