1 Mbiri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ku Yerusalemu+ kunkakhala ana ena a Yuda,+ Benjamini,+ Efuraimu ndi Manase.