1 Mbiri 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panalinso abale awo. Onse anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo, ndipo analipo 1,760. Iwo anali amuna amphamvu, omwe anali kugwira ntchito+ yotumikira panyumba ya Mulungu woona.
13 Panalinso abale awo. Onse anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo, ndipo analipo 1,760. Iwo anali amuna amphamvu, omwe anali kugwira ntchito+ yotumikira panyumba ya Mulungu woona.