Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno asilikali othamanga+ amene anatenga makalata ochokera kwa mfumu ndi kwa akalonga ake,+ anapita mu Isiraeli ndi Yuda yense mogwirizana ndi lamulo la mfumu, lakuti: “Inu ana a Isiraeli, bwererani+ kwa Yehova Mulungu+ wa Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli, kuti iye abwerere kwa anthu anu otsala+ amene anapulumuka m’manja mwa mafumu a Asuri.+

  • Esitere 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Amtokomawo+ anathamanga ndi kupita mofulumira atakwera pamahatchi amene anali kuwagwiritsa ntchito potumikira mfumu. Anapita mofulumira+ chifukwa cha mawu a mfumu ndipo lamulo linachokera m’nyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.+

  • Yeremiya 51:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Munthu mmodzi wothamanga wakumana ndi mnzake, ndipo mthenga mmodzi wakumana ndi mnzake,+ onsewa akukanena kwa mfumu ya Babulo kuti mzinda wake walandidwa kumbali zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena