Esitere 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mfumukazi Vasiti inakana+ kubwera itaitanidwa ndi mfumu kudzera mwa nduna za panyumba ya mfumu. Pamenepo mfumu inakwiya kwambiri ndipo mumtima mwake munali ukali waukulu.+ Esitere 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pambuyo pake, mkwiyo wa Mfumu Ahasiwero+ utachepa, iye anakumbukira Vasiti+ ndi zimene anachita,+ komanso chilango chimene anasankha kum’patsa.+ Esitere 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mfumu inakonda kwambiri Esitere kuposa akazi ena onse, moti mfumu inakondwera naye ndipo inamusonyeza kukoma mtima kosatha kuposa anamwali ena onse.+ Pamenepo mfumu inamuveka duku lachifumu kumutu kwake ndi kumusandutsa mfumukazi+ m’malo mwa Vasiti.
12 Koma Mfumukazi Vasiti inakana+ kubwera itaitanidwa ndi mfumu kudzera mwa nduna za panyumba ya mfumu. Pamenepo mfumu inakwiya kwambiri ndipo mumtima mwake munali ukali waukulu.+
2 Pambuyo pake, mkwiyo wa Mfumu Ahasiwero+ utachepa, iye anakumbukira Vasiti+ ndi zimene anachita,+ komanso chilango chimene anasankha kum’patsa.+
17 Ndiyeno mfumu inakonda kwambiri Esitere kuposa akazi ena onse, moti mfumu inakondwera naye ndipo inamusonyeza kukoma mtima kosatha kuposa anamwali ena onse.+ Pamenepo mfumu inamuveka duku lachifumu kumutu kwake ndi kumusandutsa mfumukazi+ m’malo mwa Vasiti.