Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 24:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,

      Ndipo mbewu yake ili m’mbali mwa madzi ambiri.+

      Mfumu yakenso+ idzakwezeka kuposa Agagi,+

      Ndi ufumu wake udzakwezedwa.+

  • Deuteronomo 25:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.

  • 1 Samueli 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iye anagwira Agagi+ mfumu ya Amaleki ali wamoyo, ndipo anthu ena onse anawapha ndi lupanga.+

  • Esitere 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata+ Mwagagi,+ amene anali kudana+ ndi Ayuda onse, anakonzera Ayudawo chiwembu kuti awawononge.+ Choncho iye anachita Puri+ kapena kuti Maere,+ ndi cholinga chakuti awasautse ndi kuwawononga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena