Salimo 92:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Diso langa lidzayang’ana adani anga atagonja,+Makutu anga adzamva za anthu ondiukira, anthu ochita zoipa. Salimo 149:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuti abwezere anthu a mitundu ina,+Ndi kudzudzula mitundu ya anthu,+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
11 Diso langa lidzayang’ana adani anga atagonja,+Makutu anga adzamva za anthu ondiukira, anthu ochita zoipa.
7 Kuti abwezere anthu a mitundu ina,+Ndi kudzudzula mitundu ya anthu,+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?