Salimo 145:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo,+Ndipo adzasimba za zochita zanu zamphamvu.+