Esitere 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti zimene mfumukazi yachita zidziwika kwa akazi onse okwatiwa ndipo iwo ayamba kunyoza+ amuna awo+ ponena kuti, ‘Mfumu Ahasiwero inalamula kuti Mfumukazi Vasiti ibwere pamaso pake koma Vasiti sanapite.’
17 Pakuti zimene mfumukazi yachita zidziwika kwa akazi onse okwatiwa ndipo iwo ayamba kunyoza+ amuna awo+ ponena kuti, ‘Mfumu Ahasiwero inalamula kuti Mfumukazi Vasiti ibwere pamaso pake koma Vasiti sanapite.’