Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Mlendo wokhala pakati panu muzimuona ngati mbadwa. Muzim’konda mmene mumadzikondera nokha,+ chifukwa inunso munali alendo m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

  • Levitiko 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+

  • Rute 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Rute anati: “Musandichonderere kuti ndikusiyeni, kuti ndibwerere ndisakutsatireni, pakuti kumene inu mupite inenso ndipita komweko, kumene inu mugone inenso ndigona komweko.+ Anthu a mtundu wanu adzakhala anthu a mtundu wanga,+ ndipo Mulungu wanu adzakhala Mulungu wanga.+

  • 1 Mafumu 8:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika,+ ndipo muchite mogwirizana ndi zonse zimene mlendoyo wakupemphani.+ Mutero n’cholinga choti anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi adziwe dzina lanu,+ kuti akuopeni mofanana ndi mmene anthu anu Aisiraeli amachitira, ndiponso kuti adziwe kuti dzina lanu lili panyumba imene ndamangayi.+

  • Esitere 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 M’zigawo zonse ndi m’mizinda yonse kumene mawu a mfumu ndi lamulo lake linafika, Ayuda anali kusangalala ndi kukondwera. Anachita phwando+ ndipo linali tsiku lachisangalalo. Anthu ambiri+ a m’dzikomo anayamba kudzitcha Ayuda+ chifukwa anali kuchita mantha kwambiri+ ndi Ayudawo.

  • Agalatiya 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kuwonjezera apo, ndikunenetsa kwa munthu aliyense amene akudulidwa, kuti afunikanso kuchita zonse za m’Chilamulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena