Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+ Maliro 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+
10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+