Yesaya 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usachite mantha,+ pakuti sudzachititsidwa manyazi.+ Usachite manyazi, pakuti sudzakhumudwitsidwa.+ Iwe udzaiwala ngakhale manyazi a paubwana wako,+ ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako wa nthawi yaitali.”
4 Usachite mantha,+ pakuti sudzachititsidwa manyazi.+ Usachite manyazi, pakuti sudzakhumudwitsidwa.+ Iwe udzaiwala ngakhale manyazi a paubwana wako,+ ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako wa nthawi yaitali.”