Esitere 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nayonso Mfumukazi Vasiti+ inakonzera phwando akazi kunyumba ya Mfumu Ahasiwero.