Numeri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,Ndipo mbewu yake ili m’mbali mwa madzi ambiri.+Mfumu yakenso+ idzakwezeka kuposa Agagi,+Ndi ufumu wake udzakwezedwa.+ 1 Samueli 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anagwira Agagi+ mfumu ya Amaleki ali wamoyo, ndipo anthu ena onse anawapha ndi lupanga.+ 1 Samueli 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Samueli anati: “M’bweretseni kuno Agagi mfumu ya Amaleki.” Atatero, Agagi anapita kwa Samueli mwamantha ndi mokayikira.* Mumtima mwake Agagi anayamba kunena kuti: “Ndithudi, ululu wa imfa wachoka.”
7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,Ndipo mbewu yake ili m’mbali mwa madzi ambiri.+Mfumu yakenso+ idzakwezeka kuposa Agagi,+Ndi ufumu wake udzakwezedwa.+
32 Kenako Samueli anati: “M’bweretseni kuno Agagi mfumu ya Amaleki.” Atatero, Agagi anapita kwa Samueli mwamantha ndi mokayikira.* Mumtima mwake Agagi anayamba kunena kuti: “Ndithudi, ululu wa imfa wachoka.”