Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+

      Mawu anga adzatsika ngati mame,+

      Ngati mvula yowaza pa udzu,+

      Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+

  • Miyambo 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chifukwa chakuti iye amadziwa zinthu, anagawa madzi akuya,+ ndipo kumwamba kwa mitambo kumagwetsa mvula yamawawa.+

  • Yesaya 55:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti monga momwe mvula ndi chipale chofewa zimagwera kuchokera kumwamba, osabwereranso kumeneko mpaka zitanyowetsa kwambiri nthaka n’kumeretsa zomera ndi kuzibereketsa,+ wobzala mbewu n’kupatsidwa zokolola komanso wakudya n’kupatsidwa chakudya,+

  • Yeremiya 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi pakati pa mafano opanda pake a mitundu ya anthu pali fano lililonse+ limene lingagwetse mvula? Kapena kodi kumwamba pakokha kungagwetse mvula yamvumbi?+ Kodi si inu Yehova Mulungu wathu+ amene mumachititsa zimenezi? Chiyembekezo chathu chili mwa inu chifukwa ndinu amene mumachititsa zonsezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena