Salimo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Thyolani dzanja la woipa ndi wankhanzayo.+Fufuzani zoipa zake zonse ndi kumulanga kufikira zoipazo zitatha.+ Yeremiya 48:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘Nyanga* ya Mowabu yadulidwa+ ndipo dzanja lake lathyoledwa,’+ watero Yehova. Ezekieli 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndithana ndi Farao mfumu ya Iguputo.+ Ndidzathyola manja ake onse,+ dzanja lamphamvu ndi lothyoka lija,+ ndipo ndidzachititsa kuti lupanga ligwe m’dzanja lake.+
15 Thyolani dzanja la woipa ndi wankhanzayo.+Fufuzani zoipa zake zonse ndi kumulanga kufikira zoipazo zitatha.+
22 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndithana ndi Farao mfumu ya Iguputo.+ Ndidzathyola manja ake onse,+ dzanja lamphamvu ndi lothyoka lija,+ ndipo ndidzachititsa kuti lupanga ligwe m’dzanja lake.+