Yobu 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwala kwa oipa kumachotsedwa,+Ndipo dzanja lokwezedwa m’mwamba limathyoledwa.+ Salimo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Thyolani dzanja la woipa ndi wankhanzayo.+Fufuzani zoipa zake zonse ndi kumulanga kufikira zoipazo zitatha.+ Salimo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti manja a anthu oipa adzathyoledwa,+Koma Yehova adzathandiza anthu olungama.+ Ezekieli 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzathyola dzanja la Farao mfumu ya Iguputo.+ Dzanjalo silidzamangidwa ndi nsalu zomangira pachilonda+ kuti lichire n’kukhalanso lamphamvu kuti lizidzatha kugwira lupanga.”
15 Thyolani dzanja la woipa ndi wankhanzayo.+Fufuzani zoipa zake zonse ndi kumulanga kufikira zoipazo zitatha.+
21 “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzathyola dzanja la Farao mfumu ya Iguputo.+ Dzanjalo silidzamangidwa ndi nsalu zomangira pachilonda+ kuti lichire n’kukhalanso lamphamvu kuti lizidzatha kugwira lupanga.”