Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+ Yobu 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ine tsopano ndakhala wopanda pake.+Kodi ndingakuyankheni chiyani?Ndaika dzanja langa pakamwa.+ Salimo 51:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kudzimvera chisoni mumtima ndizo nsembe zimene Mulungu amavomereza.+Inu Mulungu, simudzanyoza mtima wosweka ndi wophwanyika.+
6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+
17 Kudzimvera chisoni mumtima ndizo nsembe zimene Mulungu amavomereza.+Inu Mulungu, simudzanyoza mtima wosweka ndi wophwanyika.+