Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iwo anamuyankha kuti: “Khala chete. Gwira pakamwa pako, ndipo upite nafe kuti ukakhale tate+ ndi wansembe+ wathu. Chabwino n’chiti, kuti upitirize kukhala wansembe m’nyumba ya munthu mmodzi,+ kapena kuti ukhale wansembe wa banja ndi fuko lonse mu Isiraeli?”+

  • Yobu 29:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Akalonga ankabweza mawu,

      Ndipo ankagwira pakamwa.+

  • Salimo 39:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ndinakhala chete.+ Sindinatsegule pakamwa panga,+

      Pakuti inu munachitapo kanthu.+

  • Miyambo 30:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ngati wachita zinthu zopusa n’kudzikweza,+ ndiponso ngati watsimikiza mtima wako kuti uchite zimenezo, gwira pakamwa pako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena