Yobu 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 N’chifukwa chiyani simukundikhululukira machimo anga,+Ndi kunyalanyaza zolakwa zanga?Pakuti tsopano ndigona m’fumbi.+Mudzandifunafuna koma ine kudzakhala kulibe.” Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
21 N’chifukwa chiyani simukundikhululukira machimo anga,+Ndi kunyalanyaza zolakwa zanga?Pakuti tsopano ndigona m’fumbi.+Mudzandifunafuna koma ine kudzakhala kulibe.”
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+