Yesaya 64:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+
8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+