Yobu 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masiku anga akufulumira+ kuposa mmene chimathamangira chowombera nsalu,Iwo afika pamapeto popanda chiyembekezo.+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+ Salimo 39:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.] Salimo 103:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+
6 Masiku anga akufulumira+ kuposa mmene chimathamangira chowombera nsalu,Iwo afika pamapeto popanda chiyembekezo.+
5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.]
15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+