Salimo 94:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amadziwa kuti maganizo a anthu ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ Zefaniya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anali wolungama mkati mwa mzindawo+ ndipo sanali kuchita zosalungama.+ M’mawa uliwonse iye anali kuchita chilungamo chake+ moti sichinali kusowa mpaka m’bandakucha,+ koma wosalungamayo sanali kuchita manyazi.+
5 Yehova anali wolungama mkati mwa mzindawo+ ndipo sanali kuchita zosalungama.+ M’mawa uliwonse iye anali kuchita chilungamo chake+ moti sichinali kusowa mpaka m’bandakucha,+ koma wosalungamayo sanali kuchita manyazi.+