Levitiko 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+ Salimo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndidzagona pansi ndi kupeza tulo.Ndidzadzuka ndithu, pakuti Yehova amandithandiza.+ Miyambo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nthawi iliyonse ukagona sudzaopa chilichonse.+ Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+
6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+
24 Nthawi iliyonse ukagona sudzaopa chilichonse.+ Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+