Yeremiya 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Tchimo la Yuda lalembedwa ndi chitsulo chogobera.+ Lalembedwa ndi cholembera cha dayamondi m’mitima+ yawo ndi panyanga za guwa lansembe.+
17 “Tchimo la Yuda lalembedwa ndi chitsulo chogobera.+ Lalembedwa ndi cholembera cha dayamondi m’mitima+ yawo ndi panyanga za guwa lansembe.+