Yesaya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi anafunsirapo nzeru kwa ndani kuti amuthandize kumvetsetsa zinthu? Ndani amamuphunzitsa njira ya chilungamo? Ndani amamuphunzitsa kuti azidziwa zinthu,+ ndipo ndani amamuphunzitsa kuti akhale womvetsa bwino zinthu?+ Aroma 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova,+ kapena ndani angakhale phungu wake?”+ 1 Akorinto 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova+ kuti amulangize?”+ Koma ifeyo tili ndi maganizo+ a Khristu.
14 Kodi anafunsirapo nzeru kwa ndani kuti amuthandize kumvetsetsa zinthu? Ndani amamuphunzitsa njira ya chilungamo? Ndani amamuphunzitsa kuti azidziwa zinthu,+ ndipo ndani amamuphunzitsa kuti akhale womvetsa bwino zinthu?+
16 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova+ kuti amulangize?”+ Koma ifeyo tili ndi maganizo+ a Khristu.