Salimo 109:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+ Miyambo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene amabera mwachinyengo munthu wonyozeka kuti apeze zinthu zambiri,+ komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera, ndithu adzasauka.+ Yesaya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+ Amosi 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani izi amuna inu, inu amene mukufuna kumeza munthu wosauka+ ndiponso amene mukufuna kufafaniza anthu ofatsa padziko lapansi.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.
16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+
16 Amene amabera mwachinyengo munthu wonyozeka kuti apeze zinthu zambiri,+ komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera, ndithu adzasauka.+
2 Iwo amachita zimenezi n’cholinga choti asamvetsere mlandu wa anthu onyozeka ndiponso kuti anthu anga osautsika awalande chilungamo.+ Amateronso kuti atenge akazi amasiye ngati katundu wolanda ndiponso kuti atenge ana amasiye.*+
4 “Tamverani izi amuna inu, inu amene mukufuna kumeza munthu wosauka+ ndiponso amene mukufuna kufafaniza anthu ofatsa padziko lapansi.+
4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.