Yobu 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Zoonadi, amuna inu ndinu anthu,Ndipo nzeru zidzathera limodzi ndi inu.+ Yobu 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi umamvetsera nkhani zachinsinsi za Mulungu?+Ndipo kodi umaona kuti iwe wekha ndiye wanzeru? Yobu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komabe, amuna nonsenu mungathe kuyambiranso kundinena. Chotero pitirizani,Chifukwa sindikuonapo wanzeru pakati panu.+
10 Komabe, amuna nonsenu mungathe kuyambiranso kundinena. Chotero pitirizani,Chifukwa sindikuonapo wanzeru pakati panu.+