Yobu 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Kodi ungawedze ng’ona*+ ndi mbedza?Kapena ungamange lilime lake ndi chingwe? Yobu 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Palibe angalimbe mtima kuti aipute.Kodi ndani angaimitsane nane?+ Salimo 74:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu munaphwanya mitu ya Leviyatani*+ kukhala zidutswazidutswa.Munaipereka kwa anthu monga chakudya, munaipereka kwa anthu okhala m’madera opanda madzi.+ Salimo 104:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zombo zimayenda mmenemo.+Ndipo Leviyatani*+ munam’panga kuti azisewera mmenemo.+
14 Inu munaphwanya mitu ya Leviyatani*+ kukhala zidutswazidutswa.Munaipereka kwa anthu monga chakudya, munaipereka kwa anthu okhala m’madera opanda madzi.+