Yobu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chonde sinthani maganizo anu, kuti pachitike chilungamo.Ndithu sinthani maganizo. Inetu ndikadali wolungama.+ Yobu 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndagwira chilungamo changa ndipo sindichitaya.+Mtima wanga sudzandinyoza masiku anga onse.+ Miyambo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usamadzione kuti ndiwe wanzeru.+ Uziopa Yehova ndi kupatuka pa choipa.+
29 Chonde sinthani maganizo anu, kuti pachitike chilungamo.Ndithu sinthani maganizo. Inetu ndikadali wolungama.+