Miyambo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo. Yesaya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsoka kwa amene amadziona ngati anzeru komanso amadziyesa ochenjera.+ Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+
12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo.
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+