Salimo 146:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+ Mlaliki 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+ Yesaya 57:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amalowa mumtendere.+ Aliyense woyenda mowongoka+ amapita kukapuma+ m’manda.*+
4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+
10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+