Yobu 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo amafa mwadzidzidzi,+ ngakhale pakati pa usiku.+Anthuwo amagwedezeka uku ndi uku n’kufa,Ndipo amphamvu amachoka popanda dzanja lowachotsa.+ Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
20 Iwo amafa mwadzidzidzi,+ ngakhale pakati pa usiku.+Anthuwo amagwedezeka uku ndi uku n’kufa,Ndipo amphamvu amachoka popanda dzanja lowachotsa.+
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+