Salimo 92:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ntchito zanu ndi zazikuludi inu Yehova!+Maganizo anu ndi ozama kwambiri.+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+