Malaki 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+ Mateyu 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+
18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+
2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+