Salimo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+ Yesaya 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Ife tikudalira inu.+ Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ m’mawa uliwonse.+ Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi ya masautso.+
9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+
2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Ife tikudalira inu.+ Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ m’mawa uliwonse.+ Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi ya masautso.+