Salimo 39:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.]
11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.]