Yobu 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ine* ndili ngati chinthu chowola chimene chimatha.+Ngati chovala chimene njenjete* zimadya.+ Yesaya 50:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza. Ndani amene anganene kuti ndine wolakwa?+ Onsewo adzatha ngati chovala.+ Njenjete* idzawadya.+ Yesaya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti njenjete idzawadya ngati chovala ndipo kachilombo kodya zovala kadzawadya ngati thonje.+ Koma chilungamo changa chidzakhala mpaka kalekale ndipo chipulumutso changa chidzafikira mibadwo yosawerengeka.”+ Hoseya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndinali ngati njenjete*+ kwa Efuraimu, ndiponso ndinachititsa kuti nyumba ya Yuda iwole.
9 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza. Ndani amene anganene kuti ndine wolakwa?+ Onsewo adzatha ngati chovala.+ Njenjete* idzawadya.+
8 Pakuti njenjete idzawadya ngati chovala ndipo kachilombo kodya zovala kadzawadya ngati thonje.+ Koma chilungamo changa chidzakhala mpaka kalekale ndipo chipulumutso changa chidzafikira mibadwo yosawerengeka.”+