Salimo 108:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.+Ulemerero wanu ukhale pamwamba pa dziko lonse lapansi.+ Salimo 113:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova wakwezeka pamwamba pa mitundu yonse ya anthu.+Ulemerero wake uli pamwamba pa kumwamba.+
5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.+Ulemerero wanu ukhale pamwamba pa dziko lonse lapansi.+