Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+ Salimo 57:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.+Ulemerero wanu ukhale pamwamba pa dziko lonse lapansi.+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+
5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.+Ulemerero wanu ukhale pamwamba pa dziko lonse lapansi.+