Salimo 18:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+ Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+
50 Iye akuchita ntchito zazikulu za chipulumutso kwa mfumu yake,+Ndipo akusonyeza kukoma mtima kosatha kwa wodzozedwa wake,+kwa Davide ndi mbewu yake mpaka kalekale.+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale.+Nthawi zonse pamene dzuwa latuluka, dzina lake lizitchuka,Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.*+Mitundu yonse ya anthu imutche wodala.+