Salimo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti mtima wanga uimbe nyimbo zokutamandani ndipo usakhale chete.+Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.+ Salimo 145:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Salimo 146:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+
12 Kuti mtima wanga uimbe nyimbo zokutamandani ndipo usakhale chete.+Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.+
145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+