Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+

      Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+

      Ndipo inu mudzawateteza.

      Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+

  • Salimo 32:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+

      Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+

  • Salimo 36:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Mulungu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwamtengo wapatali!+

      Ndipo ana a anthu amabisala mu mthunzi wa mapiko anu.+

  • Salimo 57:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+

      Pakuti ine ndathawira kwa inu.+

      Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+

  • Salimo 61:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndidzakhala mlendo m’chihema chanu mpaka kalekale.+

      Ndidzathawira m’malo obisalamo kunsi kwa mapiko anu.+ [Seʹlah.]

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena