Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+ Yesaya 45:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tembenukirani kwa ine kuti mupulumuke,+ inu nonse amene muli kumapeto kwa dziko lapansi, pakuti ine ndine Mulungu ndipo palibenso wina.+
27 Anthu onse okhala kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova ndi kubwerera kwa iye.+Ndipo mafuko onse a anthu a mitundu ina adzagwada pamaso panu.+
22 “Tembenukirani kwa ine kuti mupulumuke,+ inu nonse amene muli kumapeto kwa dziko lapansi, pakuti ine ndine Mulungu ndipo palibenso wina.+