Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+ Salimo 85:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mupitiriza kutikwiyira mpaka kalekale?+Kodi mudzasonyeza mkwiyo wanu ku mibadwomibadwo?+ Maliro 3:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mwadzitchinga ndi mtambo waukulu+ kuti pemphero lisadutse ndi kufika kwa inu.+
74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+