Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo ndinayankha mfumuyo kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Kodi nkhope yanga ilekerenji kukhala yachisoni pamene mzinda+ umene makolo anga+ anaikidwako uli bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto?”+

  • Nehemiya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho tinapitiriza kumanga mpandawo, ndipo khoma lonse linalumikizana mpaka kufika hafu ya kutalika kwake. Anthu anapitiriza kukhala ndi mtima wogwira ntchito.+

  • Salimo 137:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndikakuiwala iwe Yerusalemu,+

      Dzanja langa lamanja liiwale luso lake.

  • Danieli 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Inu Yehova, nthawi zonse mumachita zinthu zolungama.+ Chonde, chotsani mkwiyo wanu waukulu pa Yerusalemu, phiri lanu loyera.+ Pakuti chifukwa cha machimo athu ndi zolakwa za makolo athu,+ Yerusalemu ndi anthu anu takhala chinthu chotonzedwa ndi anthu onse otizungulira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena