2 Mafumu 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amaziya anapha Aedomu+ okwana 10,000 m’chigwa cha Mchere+ n’kulanda mzinda wa Sela pankhondo. Kenako mzindawo anayamba kuutcha Yokiteeli ndipo dzina lake ndi lomweli mpaka lero. Obadiya 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’
7 Amaziya anapha Aedomu+ okwana 10,000 m’chigwa cha Mchere+ n’kulanda mzinda wa Sela pankhondo. Kenako mzindawo anayamba kuutcha Yokiteeli ndipo dzina lake ndi lomweli mpaka lero.
3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’